Deuteronomy 2:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Chauta, Mulungu wathu, adampereka kwa ife, ndipo tidamgonjetsa iyeyo pamodzi ndi ana ake ndi anthu ake omwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova Mulungu wathu anampereka iye pamaso pathu; ndipo tinamkantha, iye ndi ana ake amuna ndi anthu ake onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova Mulungu anamupereka iye kwa ife ndipo tinankantha, pamodzi ndi ana ake aamuna ndi gulu lake lonse lankhondo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova Mulungu wathu anampereka iye pamaso pathu; ndipo tinamkantha, iye ndi ana ace amuna ndi anthu ace onse.