Deuteronomy 2:35 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ng'ombe zokha tidasunga ngati zofunkha zathu, pamodzi ndi chuma cha m'mizinda imene tidalandayo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zoweta zokha tinadzifunkhira, pamodzi ndi zofunkha za midzi tidailanda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ziweto ndi zinthu zonse zimene tinalanda mʼmizinda imene tinagonjetsayo, tinazitenga kukhala zathu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zoweta zokha tinadzifunkhira, pamodzi ndi zofunkha za midzi tidailanda.