Deuteronomy 2:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulangize anthu kuti: Muli pafupi kubzola dziko la achibale anu, zidzukulu za Esau, amene akukhala m'Seiri. Iwowo adzakuwopani inu, koma inu muchenjere,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo uuze anthu, ndi kuti, Mukapite kubzola malire a abale anu, ana a Esau okhala m'Seiri; ndipo adzakuopani; muchenjere ndithu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Apatse anthu malamulo awa: ‘Muli pafupi kudutsa mʼchigawo cha abale anu adzukulu a Esau okhala ku Seiri. Iwowa adzachita nanu mantha koma musamale kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo uuze anthu, ndi kuti, Mukapite kubzyola malire a abale anu, ana a Bsau okhala m'Seiri; ndipo adzakuopani; mucenjere ndithu;