Deuteronomy 2:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chakudya mudzachita chogula ndi ndalama, madzi akumwanso mudzachita ogula ndi ndalama.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mugulane nao chakudya ndi ndalama, kuti mudye; mugulane naonso madzi kuti mumwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu muyenera kuwalipira ndi siliva pa chakudya chimene mudye ndi madzi amene mumwe.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mugulane nao cakudya ndi ndarama, kuti mudye; mugulane naonso madzi kuti mumwe.