Deuteronomy 20:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mukamapita kukathira nkhondo mzinda, poyamba apatseni anthu amumzindawo mwai woti agonje okha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene muyandikiza mudzi kuchita nao nkhondo, muziufuulira ndi mtendere.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene mukuyandikira kuphwanya mzinda, muyambe mwafunsa anthu a mu mzindawo ngati afuna zamtendere.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamene muyandikiza mudzi kucita nao nkhondo, muziupfuulira ndi mtendere.