Deuteronomy 20:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akakutsekulirani zipata nakugonjerani, akhale akapolo anu onsewo, ndipo akugwirireni ntchito yaukapolo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kudzali, ukakubwezerani mau a mtendere, ndi kukutsegulirani, pamenepo anthu onse opereka m'mwemo akhale akapolo anu, nadzakugwirirani ntchito yathangata.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akavomera natsekula zipata zawo, anthu wonse mu mzindawo adzagwidwa ukapolo nakugwirirani ntchito.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kudzali, ukakubwezerani mau a mtendere, ndi kukutsegulirani, pamenepo anthu onse opereka m'mwemo akhale alambi anu, nadzakutumikirani.