Deuteronomy 20:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ngati anthu a mu mzinda umenewo akana kugonja, nasankhula nkhondo, uzingeni mzindawo ndi gulu lanu lankhondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ukapanda kuchita zamtendere ndi inu, koma kuchita nkhondo nanu, pamenepo muumangire tsasa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma akakana za mtendere nachita nanu nkhondo, muwuphwanye mzindawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ukapanda kucita zamtendere ndi inu, koma kucita nkhondo nanu, pamenepo uumangire tsasa.