Deuteronomy 20:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma akazi ndi ana mungoŵagwira, ndipo mutengenso zoŵeta ndi zonse zimene zili mumzindamo ngati zofunkha zanu. Zinthu zonse za adani anu muzigwiritse ntchito, Chauta wakupatsani zimenezo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma akazi ndi ana ndi ng'ombe ndi zonse zili m'mudzimo, zankhondo zake zonse, mudzifunkhire nokha; ndipo mudye zankhondo za adani anu, zimene Yehova Mulungu wanu anakupatsani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akazi, ana, ziweto ndi china chilichonse mu mzindamo, mukhoza kuzitenga kuti zikhale zanu monga katundu wolanda ku nkhondo. Katundu wa adani anuyu amene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, mukhoza kumugwiritsa ntchito.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma akazi ndi ana ndi ng'ombe ndi zonse ziti m'mudzimo, zankhondo zace zonse, mudzifunkhire nokha; ndipo mudye zankhondo za adani anu, zimene Yehova Mulungu wanu anakupatsani.