Deuteronomy 20:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Umu ndi m'mene muzikachitira ndi mizinda ya kutali ndi inu, imene siili mizinda ya anthu akuno.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Muzitero nayo midzi yonse yokhala kutalitali ndi inu, yosakhala midzi ya amitundu awa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mizinda yonse yakutali osati ya mitundu yapafupi, muzichita nayo chomwechi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Muzitero nayo midzi yonse yokhala kutaritari ndi inu, yosakhala midzi ya amitundu awa.