Deuteronomy 20:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mukadzalanda mizinda imene ili m'dziko limene Chauta, Mulungu wanu, akukupatsaniyo, muphe aliyense.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma za midzi ya amitundu awa, imene Yehova Mulungu wanu akupatsani, ikhale cholowa chanu, musasiyepo chamoyo chilichonse chakupuma;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe mʼmizinda imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani ngati cholowa chanu, musasiyemo chamoyo chilichonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma za midzi ya amitundu awa, imene Yehova Mulungu wanu akupatsani, ikhale colowa canu, musasiyepo camoyo ciri conse cakupuma;