Deuteronomy 20:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iphani onse, kuti angadzakuchimwitseni kuchimwira Chauta, Mulungu wanu, pokuphunzitsani zoipa zimene iwowo amachita akamapembedza milungu yao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti angakuphunzitseni kuchita monga mwa zonyansa zao zonse, amazichitira milungu yao; ndipo mungachimwire Yehova Mulungu wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mukapanda kutero adzakuphunzitsani kuti mutengere zinthu zonyansa zimene amachita popembedza milungu yawo ndipo mudzachimwira Yehova Mulungu wanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti angakuphunzitseni kucita monga mwa zonyansa zao zonse, amazicitira milungu yao; ndipo mungacimwire Yehova Mulungu wanu.