Deuteronomy 21:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'dziko limene Chauta, Mulungu wanu, akukupatsani kuti likhale lanulanu mwina mwake mungathe kupeza munthu wakufa m'munda, inu osadziŵa amene wamupha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akapeza munthu waphedwa m'dziko limene Yehova Mulungu wanu akupatsani likhale lanulanu, nagona pamunda, wosadziwika wakumkantha,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati munthu apezeka ataphedwa mʼmunda mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kukhala lanu koma inu osadziwa amene wamupha,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akapeza munthu waphedwa m'dziko limene Yehova Mulungu wanu akupatsani likhale lanu lanu, nagona pamunda, wosadziwika wakumkantha,