Deuteronomy 21:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwina pakati pa akapolowo inu nkuwona mkazi wokongola amene mwamkonda, ndipo mufuna kumkwatira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
mukaona mwa akapolowa mkazi wokongola, mukamkhumba, ndi kufuna mumtenga akhale mkazi wanu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndiye ngati muona mkazi wokongola pakati pa ogwidwawo nakutengani mtima, mukhoza kumutenga kuti akhale mkazi wanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
mukaona mwa akapolowa mkazi wokongola, mukamkhumba, ndi kufuna kumtenga akhale mkazi wanu;