Deuteronomy 21:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pita nayeni kwanu, ndipo mkaziyo amete kumutu, ndi kutseteka makadabo ake,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pamenepo mufike naye kwanu kunyumba yanu; ndipo amete tsitsi la pamutu pake, ndi kutenga makadabo ake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mumutengere ku nyumba kwanu, kumumeta tsitsi lake, mumuwenge zikhadabo zake
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pamenepo mufike naye kwanu ku nyumba yanu; ndipo amete tsitsi la pamutu pace, ndi kuwenga makadabo ace;