Deuteronomy 21:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthuyo akatsimikiza zoti agaŵire ana akewo chuma chake, asakondere mwana wa mkazi wokondedwa koposayo, pakumpatsa gawo la mwana woyamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pamenepo kudzali, tsiku lakugawira ana ake amuna chuma chake, sangakhoze kuyesa mwana wa wokondana naye woyamba kubadwa, wosati mwana wa wodana naye, ndiye woyamba kubadwatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
akamagawa chuma chake akanali moyo kwa ana akewo, asapereke ufulu wa mwana woyamba kubadwa kwa mwana wamwamuna wa mkazi amene amamukonda mʼmalo mwa mwana wake woyamba kubadwa weniweni amene ndi mwana wamkazi amene samukonda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pamenepo kudzali, tsiku lakugawira ana ace amuna cuma cace, sangakhoze kuyesa mwana wa wokondana naye woyamba kubadwa, wosati mwana wa wodana naye, ndiye woyamba kubadwatu.