Deuteronomy 21:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Makolo ake a mwanayo amgwire ndi kupita naye kwa akuluakulu amumzinda ku chipata cha mzindawo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
azimgwira atate wake ndi mai wake, ndi kutulukira naye kwa akulu a mudzi wake, ndi ku chipata cha malo ake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
abambo ndi amayi ake amugwire ndi kupita naye kwa akuluakulu ku chipata cha mzinda wake ndipo
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
azimgwira atate wace ndi mai wace, ndi kuturukira naye kwa akuru a mudzi wace, ndi ku cipata ca malo ace;