Deuteronomy 21:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu akaphedwa chifukwa cha mlandu, ndipo mtembo wake ndi wopachikidwa pa mtengo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munthu akakhala nalo tchimo loyenera imfa, kuti amuphe, ndipo wampachika;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati munthu wopezeka ndi mlandu wopha mnzake waphedwa ndipo mtembo wake wapachikidwa pamtengo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munthu akakhala nalo cimo loyenera imfa, kuti amuphe, ndipo wampacika;