Deuteronomy 21:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo akuluakulu a mudzi woyandikana kwambiri ndi pamene pali mtembopo, asankhe ng'ombe imene sidagwirepo ntchito, ndipo sidakokepo galeta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo kudzali kuti mudzi wakukhala kufupi kwa munthu wophedwayo, inde akulu a mudzi uwu atenge ng'ombe yaikazi yosagwira ntchito, yosakoka goli;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka akuluakulu a mzinda wapafupi kwambiri ndi mtembowo adzatenge ngʼombe imene sinagwirepo ntchito kapena kuvalapo goli
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo kudzali kuti mudzi wakukhala kufupi kwa munthu wophedwayo, inde akuru a mudzi uwu atenge ng'ombe yamsoti yosagwira nchito, yosakoka goli;