Deuteronomy 22:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musamange ng'ombe ndi bulu kuti zilimire pamodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Musamalima ndi bulu ndi ng'ombe zikoke pamodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musatipule pogwiritsa ntchito ngʼombe ndi bulu pa goli limodzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Musamalima ndi buru ndi ng'ombe zikoke pamodzi.