Deuteronomy 22:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthuyo wachita kumgwira mtsikanayo nkuchita naye chigololo kuthengo. Ndipo ngakhale adaakuwa, panalibe amene akadampulumutsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti anampeza kuthengo; namwali wopalidwa bwenziyo anafuula, koma panalibe wompulumutsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pakuti mwamunayo anamupeza mtsikanayo kutchire, ndipo ngakhale mtsikana wachinkhosweyo anakuwa, panalibe anamulanditsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti anampeza kuthengo; namwali wopalidwa bwenziyo anapfuula, koma panalibe wompulumutsa.