Deuteronomy 22:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu asakwatire mkazi wa bambo wake, kapena kuchita chipongwe chomuvula.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munthu asatenge mkazi wa atate wake, kapena kuvula atate wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu asakwatire mkazi wa abambo ake pakuti ayenera kuchitira ulemu pogona pa abambo ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munthu asatenge mkazi wa atate wace, kapena kubvula atate wace.