Deuteronomy 22:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene mukumanga nyumba, muwonedi kuti mwamanga kampanda pamwamba kuzungulira mbali zonse zadenga. Apo inuyo simudzazengedwa mlandu wa kukhetsa magazi ngati wina agwa kuchokera pa denga, naphedwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene mumanga nyumba yatsopano, muzimanga kampanda pa tsindwi lake, kuti ungatengere nyumba yanu mwazi, akagwako munthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mukamanga nyumba yatsopano, mutchingire khonde lake la pa denga kuti inu musapezeke ndi mlandu wopha munthu ngati wina agwa kuchokera pa khonde la pa dengalo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamene mumanga nyumba yatsopano, muzimanga kampanda pa tsindwi lace, kuti ungatengere nyumba yanu mwazi, akagwako munthu.