Deuteronomy 23:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakati pa ana a Aisraele pasakhale akazi kapena amuna okhala mahule a ku Nyumba ya Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pasakhale mkazi wachigololo pakati pa ana akazi a Israele, kapena wachigololo pakati pa ana amuna a Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pasapezeke Mwisraeli wamwamuna kapena wamkazi wochita chiwerewere ku Nyumba ya Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pasakhale mkazi wacigololo pakati pa ana akazi a Israyeli, kapena wacigololo pakati pa ana amuna a Israyeli.