Deuteronomy 23:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ngati simulonjeza, apo palibe kulakwa ai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mukapanda kulonjeza chowinda, mulibe kuchimwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ngati mupewa kupanga mapangano simudzapezeka ochimwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mukapanda kulonieza cowinda, mulibe kucimwa.