Deuteronomy 23:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mukamayenda m'njira yodzera m'munda wamphesa wa mnzanu wokhala naye pafupi, mungathe kudyako mphesa zimene mungafune, koma musatengereko m'dengu pochoka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mukalowa m'munda wamphesa wa mnansi wanu, mudyeko mphesa ndi kukhuta nazo monga mufuna eni; koma musaika kanthu m'chotengera chanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mukalowa mʼmunda wamphesa wa mnzanu mukhoza kudya mphesa mmene mungafunire koma musayike zina mʼdengu mwanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mukalowa m'munda wamphesa wa mnansi wanu, mudyeko mphesa ndi kukhuta nazo monga mufuna eni koma musaika kanthu m'cotengera canu.