Deuteronomy 23:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa masiku onse a moyo wanu musachite kanthu kalikonse kothandiza anthu a mitundu imeneyi, kuti apeze mtendere kapena ubwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Musawafunira mtendere, kapena chowakomera masiku anu onse ku nthawi zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musachite nawo mgwirizano uliwonse wa mtendere pa moyo wanu wonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Musawafunira mtendere, kapena cowakomera masiku anu onse ku nthawi zonse.