Deuteronomy 24:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mukhale panja, mwini wakeyo achite kukupatsani yekha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Muime pabwalo, ndi munthu amene umkongoletsayo azituluka nacho chikolecho kwa inu muli pabwalo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Uziyima kunja kwa nyumba kuti munthu amene wamubwereketsa kanthuyo akubweretsere kunja komweko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Muime pabwalo, ndi munthu amene umkongoletsayo azituruka naco cikoleco kwa inu muli pabwalo.