Deuteronomy 24:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kumbukirani kuti paja mudaali akapolo ku Ejipito, ndipo kuti Chauta, Mulungu wanu, adakuwombolani kumeneko. Nchifukwa chake ndakupatsani lamulo limeneli.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma muzikumbukira kuti munali akapolo m'Ejipito, ndi kuti Yehova Mulungu wanu anakuombolaniko; chifukwa chake ndikuuzani kuchita chinthu ichi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kumbukirani kuti munali akapolo mʼdziko la Igupto ndipo Yehova Mulungu wanu anakuwombolani kumeneko. Nʼchifukwa chake ndikukulamulani kuti muzichita zimenezi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma muzikumbukila kuti munali akapolo m'Aigupto, ndi kuti Yehova Mulungu wanu anakuombolaniko; cifukwa cace ndikuuzani kucita cinthu ici.