Deuteronomy 24:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mkaziyo akakwatiwa ndi mwamuna wina,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo atatuluka m'nyumba mwake, amuke nakhale mkazi wa mwamuna wina.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mkaziyo ndi kukakwatiwa ndi mwamuna wina,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ataturuka m'nyumba mwace, amuke nakhale mkazi wa mwamuna wina.