Deuteronomy 24:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mutha kuthyola koyamba mphesa zanu, koma musapitemonso kachiŵiri m'mitengomo. Mphesa zotsalazo ndi za alendo okhala nanu, za ana amasiye ndi akazi amasiye.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mutatchera m'munda wanu wamphesa, musakunkha pambuyo panu; zikhale za mlendo, za mwana wamasiye, ndi za mkazi wamasiye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mukakolola mphesa mʼmunda mwanu musamabwereremonso kachiwiri. Zotsalazo muzilekere alendo, ana ndi akazi amasiye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mutachera m'munda wanu wamphesa, musakunkha pambuyo panu; zikhale za mlendo, za mwana wamasiye, ndi za mkazi wamasiye.