Deuteronomy 24:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mukumbukire kuti mudaali akapolo m'dziko la Ejipito. Nchifukwa chake ndakupatsani lamulo limeneli.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo muzikumbukira kuti munali akapolo m'dziko la Ejipito; chifukwa chake ndikuuzani kuchita chinthu ichi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kumbukirani kuti munali akapolo mʼdziko la Igupto. Nʼchifukwa chake ndikukulamulani kuti muzichita zimenezi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo muzikumbukila kuti munali: akapolo m'dziko la Aigupto; cifukwa cace ndikuuzani kucita cinthu ici.