Deuteronomy 26:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aejipito adatichita zankhanza ndi kutizunza potigwiritsa ntchito mwaukapolo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma Aejipito anatichitira choipa, natizunza, natisenza ntchito yolimba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Aigupto anatisautsa natizunza, kumatigwiritsa ntchito yakalavulagaga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma Aaigupto anaticitira coipa, natizunza, natisenza nchito yolimba.