Deuteronomy 26:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Potsiriza adatifikitsa kuno, natipatsa dziko lino, dziko lamwanaalirenji.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo anabwera nafe kumalo kuno, natipatsa dziko ili ndilo dziko moyenda mkaka ndi uchi ngati madzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anatibweretsa ku malo ano natipatsa dziko loyenda mkaka ndi uchi lino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo anabwera nafe kumalo kuno, natipatsa dziko ili ndilo dziko moyenda mkaka ndi uci ngati madzi.