Deuteronomy 27:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Atembereredwe aliyense wosuntha malire a mnansi wake.” Ndipo anthu onse adzayankhe kuti, “Inde, momwemo!”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wotembereredwa iye wakusendeza malire a mnansi wake. Ndi anthu onse anene, Amen.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ndi wotembereredwa munthu amene amasuntha mwala wa malire wa mnzake.” Pamenepo anthu onse adzati, “Ameni!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wotembereredwa iye wakusendeza malire a mnansi wace. Ndi anthu onse anene, Amen.