Deuteronomy 28:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mvula sidzakugwerani ndipo nthaka yanu idzauma kuti gwa ngati chitsulo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo thambo lanu la pamwamba pamutu panu lidzakhala ngati mkuwa, ndi dziko lili pansi panu ngati chitsulo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mitambo ya pamutu panu idzawuma ngati mkuwa ndipo sidzagwetsa mvula mpaka nthaka yanu idzawuma gwaa ngati chitsulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo thambo lanu la pamwamba pamutu panu lidzakhala ngati mkuwa, ndi dziko liri pansi panu ngati citsulo.