Deuteronomy 28:41 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudzabereka ana aamuna ndi aakazi ndithu, koma sadzakhala anu, chifukwa adzatengedwa ukapolo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mudzabala ana aamuna ndi aakazi, osakhala nao, popeza adzalowa ukapolo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mudzabereka ana aamuna ndi aakazi koma sadzakhala anu, chifukwa adzapita ku ukapolo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mudzabala ana amuna ndi akazi, osakhala nao, popeza adzalowa ukapolo.