Deuteronomy 28:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adzadalitsa zochita zanu zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mudzakhala odala polowa inu, mudzakhala odala potuluka inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mudzadalitsika pa kulowa kwanu ndi pa kutuluka kwanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mudzakhala odala polowa inu, mudzakhala odala poturuka inu.