Deuteronomy 29:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
zidzukulu zanu, akazi anu ndiponso alendo amene amakhala m'mahema mwanu, amene amakudulirani nkhuni ndi kumakutungirani madzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
makanda anu, akazi anu, ndi mlendo wanu wakukhala pakati pa zigono zanu, kuyambira wotema nkhuni kufikira wotunga madzi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pamodzi ndi ana ndi akazi anu, kudzanso alendo amene akukhala pakati panu omwe amakuwazirani nkhuni ndi kukutungirani madzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
makanda anu, akazi anu, ndi mlendo wanu wakukhala pakati pa zigono zanu, kuyambira wotema nkhuni kufikira wotunga madzi;