Deuteronomy 29:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chipangano chimenechi akupangana ndi munthu aliyense amene ali pano lero pamaso pa Chauta, Mulungu wathu, ndiponso ndi ena onse amene sali nafe kuno lero.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
komanso ndi iye wakuimirira pano nafe lero lino pamaso pa Yehova Mulungu wathu, ndiponso ndi iye wosakhala pano nafe lero lino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
amene muli pano pamaso pa Yehova Mulungu wathu, koma ndi iwonso amene sali pano lero.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
komanso ndi iye wakuimirira pano nafe lero lino pamaso pa Yehova Mulungu wathu, ndiponso ndi iye wosakhala pano nafe lero lino.