Deuteronomy 29:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mukudziŵa m'mene tidakhalira ku Ejipito kuja, ndiponso m'mene unaliri ulendo poyenda pakati pa maiko a mitundu ina.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mudziwa chikhalidwe chathu m'dziko la Ejipito, ndi kuti tinapyola pakati pa amitundu amene munawapyola;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu nomwe mukudziwa mmene tinkakhalira ku Igupto ndi mmene tinadutsira mayiko pa ulendo wobwera kuno.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mudziwa cikhalidwe cathu m'dziko la Aigupto, ndi kuti tinapyola pakati pa amitundu amene munawapyola;