Deuteronomy 29:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mafano ao oipa amitengo, amiyala, asiliva ndiponso agolide, amene anali pakati pao, mudaona kunyansa kwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo munapenya zonyansa zao, ndi mafano ao, mtengo ndi mwala, siliva ndi golide, zokhala pakati pao;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ife tinaona pakati pawo mafanizo ndi mafano awo onyansa, amtengo ndi amiyala, asiliva ndi agolide.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo munapenya zonyansa zao, ndi mafano ao, mtengo ndi mwala, siliva ndi golidi, zokhala pakati pao;