Deuteronomy 29:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mose adaitana Aisraele onse aja, naŵauza kuti: Paja mudadziwonera nokha zimene Chauta adachita mfumu ya ku Ejipito ndi nduna zake ndi dziko lake lonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mose anaitana Israele wonse, nati nao, Munapenya inu zonse zimene Yehova anachitira Farao, ndi anyamata ake onse, ndi dziko lake lonse, pamaso panu m'dziko la Ejipito;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mose anayitanitsa Aisraeli onse nati kwa iwo: Inu munaona zonse zimene Yehova anachita kwa Farao, nduna zake ndi dziko lake lonse ku Igupto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Mose anaitana Israyeli wonse, nati nao, Munapenya inu zonse zimene Yehova anacitira Farao, ndi anyamata ace onse, ndi dziko lace lonse, pamaso panu m'dziko la Aigupto;