Deuteronomy 29:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adzampatula pakati pa anthu a ku Israele onse ndipo adzamlanga ndi masoka potsata matemberero a chipangano olembedwa m'buku lino la malamulo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova adzamsiyanitsa ndi mafuko onse a Israele ndi kumchitira choipa, monga mwa matemberero onse a chipangano cholembedwa m'buku ili la chilamulo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova adzasankha pakati pa Aisraeli anthu oyenera masautso monga mwa matemberero onse a mʼpangano olembedwa Mʼbuku la Malamulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova adzamsiyanitsa ndi mafuko onse a Israyeli ndi kumcitira coipa, monga mwa matemberero onse a cipangano colembedwa m'buku ili la cilamulo.