Deuteronomy 29:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono dziko lonse lapansi lidzafunsa kuti, “Kodi chifukwa chiyani Chauta adachita zotere m'dziko lake? Kodi chifukwa chake chinali chiyani kuti mkwiyo wake uchite kuwopsa chotere?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
inde amitundu onse adzati, Yehova anachitira dziko ili chotero chifukwa ninji? Nchiyani kupsa mtima kwakukulu kumene?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mitundu yonse ya anthu idzafunsa kuti, “Kodi chifukwa chiyani Yehova anachita zotere mʼdziko lake? Kodi chifukwa chiyani anaonetsa mkwiyo woopsa wotere?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
inde amitundu onse adzati, Yehova anacitira dziko ili cotero cifukwa ninji? nciani kupsa mtima kwakukuru kumene?