Deuteronomy 29:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adatumikira milungu ina imene sadaipembedzepo nkale lonse, milungu imene Chauta adaŵaletsa kuipembedza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
napita natumikira milungu ina, naigwadira, milungu imene sanaidziwa, imene sanawagawira;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anachoka ndi kukatumikira milungu ina ndi kuyipembedza, milungu imene sanayidziwe, milungu imene sanawapatse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
napita natumikira milungu yina, naigwadira, milungu imene sanaidziwa, imene sanawagawira;