Deuteronomy 29:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Chauta adakwiyira anthu ake, ndipo adaŵagwetsera masoka onse olembedwa m'buku muno.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chifukwa chake Yehova anapsera mtima dziko ili kulitengera temberero lonse lolembedwa m'buku ili.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Yehova anakwiyira dziko lino, kotero anabweretsa matemberero onse amene analembedwa mʼbuku lino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
cifukwa cace Mulungu anapsera mtima dziko ili kulitengera temberero lonse lolembedwa m'buku ili.