Deuteronomy 29:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adakwiya koopsa, ndipo ali wokwiya chotero, adaŵachotseratu m'dziko lao ndi kuŵaponya m'dziko lachilendo, kumene ali lero lino.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova anawazula m'nthaka mwao mokwiya ndi mozaza, ndi m'ukali waukulu, nawaponya m'dziko lina, monga lero lino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi mkwiyo komanso ukali wake woopsa Yehova anawazula mʼdziko lawo ndi kuwaponyera mʼdziko lina, monga mmene zilili lero lino.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova anawazula m'nthaka mwao mokwiya ndi mozaza, ndi m'ukali waukuru, nawaponya m'dziko lina, monga lero lino.