Deuteronomy 29:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mpaka tsopano, Chauta sadakupatseni mtima womvetsa zinthu zimenezi, kapena maso openya, kapena makutu akumva.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma Yehova sanakupatseni mtima wakudziwa, ndi maso akupenya, ndi makutu akumva, kufikira lero lino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma mpaka lero Yehova sanakupatseni mtima wozindikira kapena maso openya kapena makutu akumva.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma Yehova sanakupatsani mtima wakudziwa, ndi maso akupenya, ndi makutu akumva, kufikira lero lino.