Deuteronomy 29:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo titafika pa malo ano, mfumu Sihoni wa ku Hesiboni, pamodzi ndi mfumu Ogi wa ku Basani, adadza kuti alimbane nafe, koma tidaŵagonjetsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene munafika pamalo pano, Sihoni mfumu ya Hesiboni, ndi Ogi mfumu ya Basani, anatuluka kudzakomana nafe kunkhondo, ndipo tinawakantha;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene munafika malo ano, Sihoni mfumu ya ku Hesiboni ndi Ogi mfumu ya ku Basani anabwera kudzamenyana nafe koma tinawagonjetsa iwo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene munafika pamalo pano, Sihoni mfumu ya Hesiboni, ndi Ogi mfumu ya Basana, anaturuka kudzakomana nafe kunkhondo, ndipo tinawakantha;