Deuteronomy 29:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tidalanda dziko lao ndi kuligaŵira mafuko a Rubeni, Gadi ndiponso hafu la fuko la Manase.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo tinalanda dziko lao, ndi kulipereka likhale cholowa chao cha Arubeni, ndi Agadi, ndi fuko la hafu la Manase.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tinatenga dziko lawo ndi kulipereka ngati cholowa cha fuko la Rubeni, fuko la Gadi ndi theka la fuko la Manase.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo tinalanda dziko lao, ndi kulipereka likhale colowa cao ca Arubeni, ndi Agadi, ndi pfuko la hafu la Manase.